Miyambo 19:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Chinthu chosiririka mwa munthu wochokera kufumbi ndicho kukoma mtima kwake kosatha,+ ndipo munthu wosauka ali bwino kuposa munthu wonama.+ Machitidwe 27:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Tsiku lotsatira tinafika ku Sidoni, ndipo Yuliyo anakomera mtima kwambiri+ Paulo ndipo anamulola kupita kwa mabwenzi ake kuti akamusamalire.+
22 Chinthu chosiririka mwa munthu wochokera kufumbi ndicho kukoma mtima kwake kosatha,+ ndipo munthu wosauka ali bwino kuposa munthu wonama.+
3 Tsiku lotsatira tinafika ku Sidoni, ndipo Yuliyo anakomera mtima kwambiri+ Paulo ndipo anamulola kupita kwa mabwenzi ake kuti akamusamalire.+