Machitidwe 24:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Choncho analamula kapitawo wa asilikali kuti amuyang’anire munthuyu ndi kumupatsako ufulu, ndi kuti asaletse munthu aliyense mwa anthu a mtundu wake kumutumikira.+
23 Choncho analamula kapitawo wa asilikali kuti amuyang’anire munthuyu ndi kumupatsako ufulu, ndi kuti asaletse munthu aliyense mwa anthu a mtundu wake kumutumikira.+