Miyambo 19:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Chinthu chosiririka mwa munthu wochokera kufumbi ndicho kukoma mtima kwake kosatha,+ ndipo munthu wosauka ali bwino kuposa munthu wonama.+ Machitidwe 28:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Pamapeto pake, titalowa mu Roma, Paulo analoledwa+ kumakhala yekha ndi msilikali womulondera.
22 Chinthu chosiririka mwa munthu wochokera kufumbi ndicho kukoma mtima kwake kosatha,+ ndipo munthu wosauka ali bwino kuposa munthu wonama.+