Genesis 18:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndiyeno Abulahamu anatenga mafuta a mkaka, mkaka, ndi ng’ombe yaing’ono yamphongo imene anakonza ija, n’kukaziika pamene panali alendowo.+ Pamene iwo anali kudya atakhala pansi pa mtengo, iye anaimirira chapafupi.+ Miyambo 30:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Pakuti mkaka ukaukhutchumula umatulutsa mafuta, mphuno ukaifinya imatulutsa magazi, ndipo kutulutsa mkwiyo kumayambitsa mkangano.+
8 Ndiyeno Abulahamu anatenga mafuta a mkaka, mkaka, ndi ng’ombe yaing’ono yamphongo imene anakonza ija, n’kukaziika pamene panali alendowo.+ Pamene iwo anali kudya atakhala pansi pa mtengo, iye anaimirira chapafupi.+
33 Pakuti mkaka ukaukhutchumula umatulutsa mafuta, mphuno ukaifinya imatulutsa magazi, ndipo kutulutsa mkwiyo kumayambitsa mkangano.+