Miyambo 26:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Monga mmene amakhalira makala pamoto wonyeka ndiponso nkhuni pamoto woyaka, ndi mmenenso amakhalira munthu wokonda kuyambana ndi anthu pokolezera mikangano.+ Miyambo 28:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Munthu wonyada amayambitsa mikangano,+ koma wodalira Yehova adzanenepa.+
21 Monga mmene amakhalira makala pamoto wonyeka ndiponso nkhuni pamoto woyaka, ndi mmenenso amakhalira munthu wokonda kuyambana ndi anthu pokolezera mikangano.+