Miyambo 3:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Usakangane ndi munthu popanda chifukwa,+ ngati sanakuchitire choipa.+ Miyambo 17:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Chiyambi cha mkangano chili ngati kuboola damu kuti madzi atulukemo.+ Choncho mkangano usanabuke, chokapo.+
14 Chiyambi cha mkangano chili ngati kuboola damu kuti madzi atulukemo.+ Choncho mkangano usanabuke, chokapo.+