Miyambo 26:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Monga mmene amakhalira makala pamoto wonyeka ndiponso nkhuni pamoto woyaka, ndi mmenenso amakhalira munthu wokonda kuyambana ndi anthu pokolezera mikangano.+
21 Monga mmene amakhalira makala pamoto wonyeka ndiponso nkhuni pamoto woyaka, ndi mmenenso amakhalira munthu wokonda kuyambana ndi anthu pokolezera mikangano.+