Miyambo 18:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Milomo ya munthu wopusa imalowa mu mkangano,+ ndipo pakamwa pake pamaitana zikwapu.+ Miyambo 20:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Kuleka kukangana kumabweretsa ulemerero kwa munthu,+ koma aliyense wopusa amafulumira kuyambitsa mkangano.+ Miyambo 25:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Usamapite kukazenga mlandu mofulumira, pakuti udzachita chiyani pamapeto pake mnzakoyo akakuchititsa manyazi?+
3 Kuleka kukangana kumabweretsa ulemerero kwa munthu,+ koma aliyense wopusa amafulumira kuyambitsa mkangano.+
8 Usamapite kukazenga mlandu mofulumira, pakuti udzachita chiyani pamapeto pake mnzakoyo akakuchititsa manyazi?+