Miyambo 14:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Wosafulumira kukwiya n’ngozindikira zinthu kwambiri,+ koma wokwiya msanga amalimbikitsa uchitsiru.+ Aefeso 4:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Koma khalani okomerana mtima,+ achifundo chachikulu,+ okhululukirana ndi mtima wonse, monga mmene inunso Mulungu anakukhululukirani ndi mtima wonse kudzera mwa Khristu.+ 2 Timoteyo 2:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Ndiponso, uzikana mafunso opusa ndi opanda nzeru,+ podziwa kuti amayambitsa mikangano.+
29 Wosafulumira kukwiya n’ngozindikira zinthu kwambiri,+ koma wokwiya msanga amalimbikitsa uchitsiru.+
32 Koma khalani okomerana mtima,+ achifundo chachikulu,+ okhululukirana ndi mtima wonse, monga mmene inunso Mulungu anakukhululukirani ndi mtima wonse kudzera mwa Khristu.+