Machitidwe 23:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Choncho panabuka phokoso lalikulu,+ ndipo alembi ena a gulu la Afarisi anaimirira ndi kuyamba kutsutsa mwaukali kuti: “Sitikupeza cholakwa chilichonse mwa munthu ameneyu.+ Koma ngati mzimu kapena mngelo walankhula naye,+ . . .”
9 Choncho panabuka phokoso lalikulu,+ ndipo alembi ena a gulu la Afarisi anaimirira ndi kuyamba kutsutsa mwaukali kuti: “Sitikupeza cholakwa chilichonse mwa munthu ameneyu.+ Koma ngati mzimu kapena mngelo walankhula naye,+ . . .”