Luka 23:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Pamenepo Pilato anauza ansembe aakulu ndi khamu la anthulo kuti: “Sindikupeza mlandu uliwonse mwa munthu uyu.”+ Machitidwe 25:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Koma ine ndinaona kuti sanachite chilichonse choyenera imfa.+ Choncho iyeyu atapempha kuti akaonekere kwa Wolemekezeka,+ ndinaganiza zomutumiza.
4 Pamenepo Pilato anauza ansembe aakulu ndi khamu la anthulo kuti: “Sindikupeza mlandu uliwonse mwa munthu uyu.”+
25 Koma ine ndinaona kuti sanachite chilichonse choyenera imfa.+ Choncho iyeyu atapempha kuti akaonekere kwa Wolemekezeka,+ ndinaganiza zomutumiza.