Machitidwe 23:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Kumeneko ndinapeza kuti akumuimba mlandu pa nkhani zokhudza Chilamulo chawo.+ Koma sanapezeke ndi mlandu uliwonse woyenera chilango cha imfa kapena kuponyedwa m’ndende.+ Machitidwe 26:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Koma pochoka anayamba kukambirana kuti: “Munthu uyu sakuchita chilichonse choyenera imfa+ kapena kumangidwa.”
29 Kumeneko ndinapeza kuti akumuimba mlandu pa nkhani zokhudza Chilamulo chawo.+ Koma sanapezeke ndi mlandu uliwonse woyenera chilango cha imfa kapena kuponyedwa m’ndende.+
31 Koma pochoka anayamba kukambirana kuti: “Munthu uyu sakuchita chilichonse choyenera imfa+ kapena kumangidwa.”