Machitidwe 23:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Kumeneko ndinapeza kuti akumuimba mlandu pa nkhani zokhudza Chilamulo chawo.+ Koma sanapezeke ndi mlandu uliwonse woyenera chilango cha imfa kapena kuponyedwa m’ndende.+ Machitidwe 25:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Koma ine ndinaona kuti sanachite chilichonse choyenera imfa.+ Choncho iyeyu atapempha kuti akaonekere kwa Wolemekezeka,+ ndinaganiza zomutumiza.
29 Kumeneko ndinapeza kuti akumuimba mlandu pa nkhani zokhudza Chilamulo chawo.+ Koma sanapezeke ndi mlandu uliwonse woyenera chilango cha imfa kapena kuponyedwa m’ndende.+
25 Koma ine ndinaona kuti sanachite chilichonse choyenera imfa.+ Choncho iyeyu atapempha kuti akaonekere kwa Wolemekezeka,+ ndinaganiza zomutumiza.