Machitidwe 25:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Koma pamene Paulo anapempha+ kuti timusunge kuti akamve chigamulo cha Wolemekezeka, ndinalamula kuti asungidwe mpaka pamene ndidzamutumize kwa Kaisara.”
21 Koma pamene Paulo anapempha+ kuti timusunge kuti akamve chigamulo cha Wolemekezeka, ndinalamula kuti asungidwe mpaka pamene ndidzamutumize kwa Kaisara.”