Machitidwe 22:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndinagwa pansi ndi kumva mawu akuti, ‘Saulo, Saulo, n’chifukwa chiyani ukundizunza?’+ Machitidwe 22:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 “Koma nditabwerera ku Yerusalemu,+ ndipo pamene ndinali kupemphera m’kachisi, ndinayamba kuona masomphenya.+
17 “Koma nditabwerera ku Yerusalemu,+ ndipo pamene ndinali kupemphera m’kachisi, ndinayamba kuona masomphenya.+