2 Akorinto 12:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ndiyenera kudzitama. Zoona, kudzitama si kopindulitsa. Koma tiyeni tisiye kaye nkhani imeneyi, tipite ku nkhani yokhudza masomphenya+ ndi mauthenga ochokera kwa Ambuye.
12 Ndiyenera kudzitama. Zoona, kudzitama si kopindulitsa. Koma tiyeni tisiye kaye nkhani imeneyi, tipite ku nkhani yokhudza masomphenya+ ndi mauthenga ochokera kwa Ambuye.