Machitidwe 2:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 ‘“Ndipo m’masiku otsiriza,” akutero Mulungu, “ndidzatsanulira mbali ya mzimu wanga+ pa anthu osiyanasiyana, ndipo ana anu aamuna ndi ana anu aakazi adzanenera. Anyamata anu adzaona masomphenya, ndipo amuna achikulire adzalota maloto.+ Machitidwe 22:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 “Koma nditabwerera ku Yerusalemu,+ ndipo pamene ndinali kupemphera m’kachisi, ndinayamba kuona masomphenya.+
17 ‘“Ndipo m’masiku otsiriza,” akutero Mulungu, “ndidzatsanulira mbali ya mzimu wanga+ pa anthu osiyanasiyana, ndipo ana anu aamuna ndi ana anu aakazi adzanenera. Anyamata anu adzaona masomphenya, ndipo amuna achikulire adzalota maloto.+
17 “Koma nditabwerera ku Yerusalemu,+ ndipo pamene ndinali kupemphera m’kachisi, ndinayamba kuona masomphenya.+