Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Timoteyo 1:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 ndiponso kuti asamamvere nkhani zonama+ ndi kukumbana mibadwo ya makolo. Zimenezi n’zosapindulitsa,+ koma zimangoyambitsa mafunso ndipo siziphunzitsa anthu chilichonse chochokera kwa Mulungu chokhudza chikhulupiriro.

  • 1 Timoteyo 4:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Koma uzipewa nkhani zonama+ zimene zimaipitsa zinthu zoyera ndi zimene amayi okalamba amakamba. M’malomwake, ukhale ndi chizolowezi chochita zinthu zokuthandiza kuti ukhalebe wodzipereka kwa Mulungu.+

  • Tito 3:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Koma iwe pewa mafunso opusa,+ kukumba mibadwo ya makolo,+ mikangano+ ndi kulimbana pa za Chilamulo,+ chifukwa zimenezi n’zosapindulitsa ndiponso n’zachabechabe.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena