1 Timoteyo 4:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Koma uzipewa nkhani zonama+ zimene zimaipitsa zinthu zoyera ndi zimene amayi okalamba amakamba. M’malomwake, ukhale ndi chizolowezi chochita zinthu zokuthandiza kuti ukhalebe wodzipereka kwa Mulungu.+ 2 Timoteyo 4:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Iwo adzasiya kumvetsera choonadi, n’kutembenukira ku nkhani zonama.+ Tito 1:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Asamasamale nthano zachiyuda+ ndi malamulo a anthu+ amene asiya choonadi.+
7 Koma uzipewa nkhani zonama+ zimene zimaipitsa zinthu zoyera ndi zimene amayi okalamba amakamba. M’malomwake, ukhale ndi chizolowezi chochita zinthu zokuthandiza kuti ukhalebe wodzipereka kwa Mulungu.+