Agalatiya 4:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Koma tsopano pamene mwadziwa Mulungu, kapena tinene kuti tsopano pamene mwadziwidwa ndi Mulungu,+ mukubwereranso bwanji ku mfundo zachibwanabwana,+ zomwe ndi zosathandiza ndiponso zopanda pake,+ n’kumafuna kukhalanso akapolo ake?+ 2 Petulo 2:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Mwambi woona uja wakwaniritsidwa pa iwo. Mwambiwo umati: “Galu+ wabwerera kumasanzi ake, ndipo nkhumba imene inasambitsidwa yapita kukagubudukanso m’matope.”+
9 Koma tsopano pamene mwadziwa Mulungu, kapena tinene kuti tsopano pamene mwadziwidwa ndi Mulungu,+ mukubwereranso bwanji ku mfundo zachibwanabwana,+ zomwe ndi zosathandiza ndiponso zopanda pake,+ n’kumafuna kukhalanso akapolo ake?+
22 Mwambi woona uja wakwaniritsidwa pa iwo. Mwambiwo umati: “Galu+ wabwerera kumasanzi ake, ndipo nkhumba imene inasambitsidwa yapita kukagubudukanso m’matope.”+