1 Timoteyo 6:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Ndithu Timoteyo, sunga bwino chimene chinaikidwa m’manja mwako.+ Pewa nkhani zopanda pake zimene zimaipitsa zinthu zoyera. Upewenso mitsutso pa zimene ena monama amati ndiye “kudziwa zinthu.”+ 2 Timoteyo 2:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Uziwakumbutsa+ zimenezi nthawi zonse. Uziwachenjeza mwamphamvu+ pamaso pa Mulungu,+ kuti asamakangane pa mawu.+ Kuchita zimenezo kulibe phindu m’pang’ono pomwe chifukwa kumawononga chikhulupiriro cha omvetsera.
20 Ndithu Timoteyo, sunga bwino chimene chinaikidwa m’manja mwako.+ Pewa nkhani zopanda pake zimene zimaipitsa zinthu zoyera. Upewenso mitsutso pa zimene ena monama amati ndiye “kudziwa zinthu.”+
14 Uziwakumbutsa+ zimenezi nthawi zonse. Uziwachenjeza mwamphamvu+ pamaso pa Mulungu,+ kuti asamakangane pa mawu.+ Kuchita zimenezo kulibe phindu m’pang’ono pomwe chifukwa kumawononga chikhulupiriro cha omvetsera.