2 Timoteyo 4:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Pamaso pa Mulungu ndi pa Khristu Yesu, amene anaikidwiratu kudzaweruza+ amoyo ndi akufa,+ akadzaonekera+ bwinobwino ndiponso akadzabwera mu ufumu wake,+ ndikukulamula mwamphamvu kuti,
4 Pamaso pa Mulungu ndi pa Khristu Yesu, amene anaikidwiratu kudzaweruza+ amoyo ndi akufa,+ akadzaonekera+ bwinobwino ndiponso akadzabwera mu ufumu wake,+ ndikukulamula mwamphamvu kuti,