Genesis 13:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Tiye tipatukane. Ukhoza kutenga mbali iliyonse ya dzikoli. Iwe ukapita kumanzere, ine ndipita kumanja, koma iwe ukapita kumanja, ine ndipita kumanzere.”+ Miyambo 25:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Usamapite kukazenga mlandu mofulumira, pakuti udzachita chiyani pamapeto pake mnzakoyo akakuchititsa manyazi?+ Mateyu 5:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Koma ine ndikukuuzani kuti: Usalimbane ndi munthu woipa, koma wina akakumenya mbama patsaya lakumanja,+ umutembenuzirenso linalo. Aroma 12:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ngati ndi kotheka, khalani mwamtendere+ ndi anthu onse, monga mmene mungathere.
9 Tiye tipatukane. Ukhoza kutenga mbali iliyonse ya dzikoli. Iwe ukapita kumanzere, ine ndipita kumanja, koma iwe ukapita kumanja, ine ndipita kumanzere.”+
8 Usamapite kukazenga mlandu mofulumira, pakuti udzachita chiyani pamapeto pake mnzakoyo akakuchititsa manyazi?+
39 Koma ine ndikukuuzani kuti: Usalimbane ndi munthu woipa, koma wina akakumenya mbama patsaya lakumanja,+ umutembenuzirenso linalo.