Miyambo 17:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Chiyambi cha mkangano chili ngati kuboola damu kuti madzi atulukemo.+ Choncho mkangano usanabuke, chokapo.+ Aroma 12:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ngati ndi kotheka, khalani mwamtendere+ ndi anthu onse, monga mmene mungathere. Aheberi 12:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Yesetsani kukhala pa mtendere ndi anthu onse,+ komanso yesetsani kukhala oyera+ chifukwa ngati munthu si woyera, sadzaona Ambuye.+
14 Chiyambi cha mkangano chili ngati kuboola damu kuti madzi atulukemo.+ Choncho mkangano usanabuke, chokapo.+
14 Yesetsani kukhala pa mtendere ndi anthu onse,+ komanso yesetsani kukhala oyera+ chifukwa ngati munthu si woyera, sadzaona Ambuye.+