Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yoswa 10:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Choncho dzuwa linaimadi, ndiponso mwezi unaima mpaka mtunduwo utalanga adani ake.+ Kodi sizinalembedwe m’buku la Yasari?+ Dzuwa linaima kumwamba pakatikati, silinafulumire kulowa pafupifupi kwa tsiku lonse lathunthu.+

  • Oweruza 11:36
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 36 Koma iye anati: “Bambo, ngati mwatsegula pakamwa panu pamaso pa Yehova, ndichitireni mogwirizana ndi zimene zatuluka pakamwa panu,+ chifukwa Yehova wakugwirirani ntchito yobwezera adani anu, ana a Amoni.”

  • Oweruza 16:28
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 28 Ndiyeno Samisoni+ anafuulira Yehova,+ kuti: “Yehova Ambuye Wamkulu Koposa, chonde, ndikumbukireni+ ndi kundipatsa mphamvu+ kamodzi kokhaka, inu Mulungu woona. Ndiloleni ndiwabwezere Afilisiti chifukwa cha limodzi mwa maso anga awiriwa.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena