Oweruza 11:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Ndiyeno Yefita analonjeza+ Yehova kuti: “Ngati mudzaperekadi ana a Amoni m’manja mwanga, Oweruza 11:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 ine ndidzapereka kwa Yehova+ aliyense amene adzatuluka m’nyumba yanga kudzandichingamira pamene ndikubwera mwamtendere+ kuchokera kwa ana a Amoni. Ndidzam’pereka monga nsembe yopsereza.”+ Aefeso 6:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ananu, muzimvera makolo anu+ mwa+ Ambuye, pakuti kuchita zimenezi n’chilungamo.+ Akolose 3:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Ananu, muzimvera+ makolo anu pa zinthu zonse, pakuti kuchita zimenezi kumakondweretsa Ambuye.
31 ine ndidzapereka kwa Yehova+ aliyense amene adzatuluka m’nyumba yanga kudzandichingamira pamene ndikubwera mwamtendere+ kuchokera kwa ana a Amoni. Ndidzam’pereka monga nsembe yopsereza.”+