Miyambo 6:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Mwana wanga, sunga lamulo la bambo ako,+ ndipo usasiye malangizo a mayi ako.+ Luka 2:51 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 51 Pamenepo ananyamuka nawo limodzi kubwerera ku Nazareti, ndipo anapitiriza kuwamvera.+ Apanso mayi akewo anasunga mosamala kwambiri mawu onsewa mumtima mwawo.+ Aefeso 6:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ananu, muzimvera makolo anu+ mwa+ Ambuye, pakuti kuchita zimenezi n’chilungamo.+
51 Pamenepo ananyamuka nawo limodzi kubwerera ku Nazareti, ndipo anapitiriza kuwamvera.+ Apanso mayi akewo anasunga mosamala kwambiri mawu onsewa mumtima mwawo.+