1 Samueli 10:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndiyeno zizindikiro+ zimenezi zikachitika pa iwe, uchite chilichonse chimene ungathe,+ chifukwa Mulungu woona ali ndi iwe.+ 1 Samueli 11:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Sauli atamva mawu amenewa mzimu+ wa Mulungu unayamba kugwira ntchito pa iye, ndipo anapsa mtima kwambiri.+ 1 Samueli 14:47 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 47 Tsopano Sauli analimbitsa ufumu wake mu Isiraeli+ ndipo anamenya nkhondo ndi adani ake onse om’zungulira. Iye anamenyana ndi Mowabu,+ ana a Amoni,+ Edomu,+ mafumu a Zoba+ ndi Afilisiti.+ Kulikonse kumene anali kutembenukira anali kuwalanga.+ 2 Samueli 1:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Uta wa Yonatani sunkalephera kupha adani ndi kukhetsa magazi awo,Sunkalephera kubaya mafuta a anthu amphamvu.+Lupanga la Sauli silinkabwerako chabe osakwaniritsa ntchito yake.+
7 Ndiyeno zizindikiro+ zimenezi zikachitika pa iwe, uchite chilichonse chimene ungathe,+ chifukwa Mulungu woona ali ndi iwe.+
6 Sauli atamva mawu amenewa mzimu+ wa Mulungu unayamba kugwira ntchito pa iye, ndipo anapsa mtima kwambiri.+
47 Tsopano Sauli analimbitsa ufumu wake mu Isiraeli+ ndipo anamenya nkhondo ndi adani ake onse om’zungulira. Iye anamenyana ndi Mowabu,+ ana a Amoni,+ Edomu,+ mafumu a Zoba+ ndi Afilisiti.+ Kulikonse kumene anali kutembenukira anali kuwalanga.+
22 Uta wa Yonatani sunkalephera kupha adani ndi kukhetsa magazi awo,Sunkalephera kubaya mafuta a anthu amphamvu.+Lupanga la Sauli silinkabwerako chabe osakwaniritsa ntchito yake.+