8 Ndipo atumiki anu onsewa adzatsika ndi kubwera kwa ine, n’kundigwadira ndi kundiweramira.+ Iwo adzanena kuti, ‘Pita, iweyo ndi anthu onse amene amakutsatira.’ Zitatero ndidzapitadi.” Atanena mawu amenewa anachoka kwa Farao atakwiya.
19 Chotero atayandikira msasawo n’kuona mwana wa ng’ombe+ ndi anthu akuvina, mkwiyo wa Mose unayaka ndipo nthawi yomweyo anaponya pansi miyala ija ndi kuiswa ali m’tsinde mwa phiri.+