-
1 Samueli 18:4Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
4 Pamenepo Yonatani anavula malaya ake akunja odula manja ndi kupatsa Davide. Anam’patsanso zovala zina ngakhalenso lupanga, uta ndi lamba wake.
-
-
1 Samueli 20:20Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
20 Ineyo ndidzaponya mivi itatu kumbali ina ya mwalawo, kuilunjikitsa pachinachake.
-