Deuteronomo 32:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Pakuti Yehova adzaweruza anthu ake,+Ndipo adzamva chisoni chifukwa cha atumiki ake,+Chifukwa adzaona kuti thandizo lawachokera.Adzaona kuti pangokhala munthu wonyozeka ndi wopanda pake. 1 Mafumu 21:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 ndikubweretsera tsoka+ ndipo ndithu ndidzaseseratu nyumba yako,+ ndi kupha munthu aliyense wokodzera khoma+ wa m’banja la Ahabu, ngakhale anthu onyozeka ndi opanda pake mu Isiraeli.
36 Pakuti Yehova adzaweruza anthu ake,+Ndipo adzamva chisoni chifukwa cha atumiki ake,+Chifukwa adzaona kuti thandizo lawachokera.Adzaona kuti pangokhala munthu wonyozeka ndi wopanda pake.
21 ndikubweretsera tsoka+ ndipo ndithu ndidzaseseratu nyumba yako,+ ndi kupha munthu aliyense wokodzera khoma+ wa m’banja la Ahabu, ngakhale anthu onyozeka ndi opanda pake mu Isiraeli.