Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Oweruza 2:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Yehova akawapatsa oweruza,+ Yehova anali kukhaladi ndi aliyense wa oweruzawo, ndipo iye anali kuwapulumutsa m’manja mwa adani awo masiku onse a moyo wa woweruzayo. Yehova anali kuchita zimenezo pakuti anali kuwamvera chisoni+ akamva kubuula kwawo chifukwa cha owapondereza ndi owakankhakankha.+

  • Salimo 90:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Bwererani kwa ife, inu Yehova!+ Kodi mudzatenga nthawi yaitali bwanji musanabwerere kwa ife?+

      Timvereni chisoni ife atumiki anu.+

  • Salimo 106:45
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 45 Zikatero anali kukumbukira pangano limene anachita ndi iwo,+

      Ndipo anali kuwamvera chisoni chifukwa cha kuchuluka kwa kukoma mtima kwake kosatha.+

  • Salimo 135:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Pakuti Yehova adzaweruzira anthu ake mlandu,+

      Ndipo adzamvera chisoni atumiki ake.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena