Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 32:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Pamenepo, Yehova anayamba kumva chisoni chifukwa cha tsoka limene ananena kuti agwetsera anthu ake.+

  • Deuteronomo 13:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Ndipo kanthu kalikonse koyenera kuwonongedwa* kasamamatire kudzanja lanu,+ kuti mkwiyo woyaka moto wa Yehova usiye kukuyakirani+ ndipo akuchitireni chifundo ndi kukumverani chisoni,+ kutinso akuchulukitseni, monga mmene analumbirira makolo anu.+

  • Deuteronomo 32:36
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 36 Pakuti Yehova adzaweruza anthu ake,+

      Ndipo adzamva chisoni chifukwa cha atumiki ake,+

      Chifukwa adzaona kuti thandizo lawachokera.

      Adzaona kuti pangokhala munthu wonyozeka ndi wopanda pake.

  • Salimo 135:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Pakuti Yehova adzaweruzira anthu ake mlandu,+

      Ndipo adzamvera chisoni atumiki ake.+

  • Amosi 7:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Yehova anamva chisoni+ ndipo Yehova anati, “Zimenezi sizidzachitika.”

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena