Ekisodo 33:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Koma Mulungu anati: “Ineyo ndidzakuonetsa ubwino wanga wonse,+ ndipo ndidzalengeza dzina langa lakuti Yehova kwa iwe.+ Amene ndikufuna kum’komera mtima ndidzam’komera mtima, ndipo amene ndikufuna kum’sonyeza chifundo, ndidzam’sonyeza chifundo.”+ Salimo 78:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Koma anawamvera chifundo.+ Anali kukhululukira* machimo awo+ ndipo sanali kuwawononga.+Nthawi zambiri anali kubweza mkwiyo wake,+Ndipo sanali kuwasonyeza ukali wake wonse.
19 Koma Mulungu anati: “Ineyo ndidzakuonetsa ubwino wanga wonse,+ ndipo ndidzalengeza dzina langa lakuti Yehova kwa iwe.+ Amene ndikufuna kum’komera mtima ndidzam’komera mtima, ndipo amene ndikufuna kum’sonyeza chifundo, ndidzam’sonyeza chifundo.”+
38 Koma anawamvera chifundo.+ Anali kukhululukira* machimo awo+ ndipo sanali kuwawononga.+Nthawi zambiri anali kubweza mkwiyo wake,+Ndipo sanali kuwasonyeza ukali wake wonse.