Yoswa 7:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Pambuyo pake, anaunjika mulu waukulu wa miyala pa iye. Muluwo ulipo mpaka lero.+ Zitatero, mkwiyo waukulu wa Yehova unatha.+ Ndiye chifukwa chake malowo anatchedwa chigwa cha Akori*+ mpaka lero. Yoswa 22:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Kodi Akani+ mwana wa Zera sanachite zosakhulupirika pa chinthu choyenera kuwonongedwa? Kodi mkwiyo sunagwere khamu lonse la Isiraeli?+ Komatu iye sanafe yekha chifukwa cha cholakwa chakecho.’”+
26 Pambuyo pake, anaunjika mulu waukulu wa miyala pa iye. Muluwo ulipo mpaka lero.+ Zitatero, mkwiyo waukulu wa Yehova unatha.+ Ndiye chifukwa chake malowo anatchedwa chigwa cha Akori*+ mpaka lero.
20 Kodi Akani+ mwana wa Zera sanachite zosakhulupirika pa chinthu choyenera kuwonongedwa? Kodi mkwiyo sunagwere khamu lonse la Isiraeli?+ Komatu iye sanafe yekha chifukwa cha cholakwa chakecho.’”+