Ekisodo 14:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Isiraeli anaonanso dzanja lamphamvu limene Yehova anagonjetsa nalo Aiguputo. Pamenepo Aisiraeli anayamba kuopa Yehova ndi kukhulupirira Yehova ndi mtumiki wake Mose.+ Salimo 7:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Yehova adzapereka chigamulo ku mitundu ya anthu.+Ndiweruzeni inu Yehova, mogwirizana ndi chilungamo changa,+Komanso mogwirizana ndi mtima wanga wosagawanika.+
31 Isiraeli anaonanso dzanja lamphamvu limene Yehova anagonjetsa nalo Aiguputo. Pamenepo Aisiraeli anayamba kuopa Yehova ndi kukhulupirira Yehova ndi mtumiki wake Mose.+
8 Yehova adzapereka chigamulo ku mitundu ya anthu.+Ndiweruzeni inu Yehova, mogwirizana ndi chilungamo changa,+Komanso mogwirizana ndi mtima wanga wosagawanika.+