Salimo 18:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Yehova amandipatsa mphoto mogwirizana ndi chilungamo changa.+Amandibwezera mogwirizana ndi kuyera kwa manja anga.+ Salimo 35:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Inu Yehova Mulungu wanga, mundiweruze mogwirizana ndi chilungamo chanu,+Musalole kuti adani anga akondwere ndi kusautsika kwanga.+
20 Yehova amandipatsa mphoto mogwirizana ndi chilungamo changa.+Amandibwezera mogwirizana ndi kuyera kwa manja anga.+
24 Inu Yehova Mulungu wanga, mundiweruze mogwirizana ndi chilungamo chanu,+Musalole kuti adani anga akondwere ndi kusautsika kwanga.+