Salimo 7:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Yehova adzapereka chigamulo ku mitundu ya anthu.+Ndiweruzeni inu Yehova, mogwirizana ndi chilungamo changa,+Komanso mogwirizana ndi mtima wanga wosagawanika.+ Salimo 26:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Ndiweruzeni,+ inu Yehova, pakuti ine ndayenda mogwirizana ndi mtima wanga wosagawanika,+Ndipo ndikudalira Yehova kuti ndisagwedezeke.+ Salimo 96:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Pakuti iye wabwera.+Iye wabwera kudzaweruza dziko lapansi.+Adzaweruza dziko mwachilungamo,+Ndipo adzaweruza mitundu ya anthu mokhulupirika.+ Yesaya 11:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Adzaweruza mwachilungamo anthu onyozeka+ ndipo adzadzudzula anthu mowongoka mtima, pothandiza ofatsa a padziko lapansi. Adzakwapula dziko lapansi ndi ndodo ya pakamwa pake,+ ndipo adzagwiritsa ntchito mzimu wa pakamwa pake kupha munthu woipa.+
8 Yehova adzapereka chigamulo ku mitundu ya anthu.+Ndiweruzeni inu Yehova, mogwirizana ndi chilungamo changa,+Komanso mogwirizana ndi mtima wanga wosagawanika.+
26 Ndiweruzeni,+ inu Yehova, pakuti ine ndayenda mogwirizana ndi mtima wanga wosagawanika,+Ndipo ndikudalira Yehova kuti ndisagwedezeke.+
13 Pakuti iye wabwera.+Iye wabwera kudzaweruza dziko lapansi.+Adzaweruza dziko mwachilungamo,+Ndipo adzaweruza mitundu ya anthu mokhulupirika.+
4 Adzaweruza mwachilungamo anthu onyozeka+ ndipo adzadzudzula anthu mowongoka mtima, pothandiza ofatsa a padziko lapansi. Adzakwapula dziko lapansi ndi ndodo ya pakamwa pake,+ ndipo adzagwiritsa ntchito mzimu wa pakamwa pake kupha munthu woipa.+