Yobu 27:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Inetu sindingayerekeze n’komwe kunena kuti amuna inu ndinu olungama.+Mpaka ine kumwalira, sindidzasiya kukhala ndi mtima wosagawanika.+ Salimo 26:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Koma ine ndidzayenda mogwirizana ndi mtima wanga wosagawanika.+Ndiwomboleni+ ndi kundikomera mtima.+ Salimo 41:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Koma ine mwandichirikiza chifukwa cha mtima wanga wosagawanika,+Ndipo mudzandiika pamaso panu mpaka kalekale.+ Salimo 78:72 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 72 Iye anayamba kuwaweta malinga ndi mtima wake wosagawanika,+Ndipo anayamba kuwatsogolera mwaluso.+ Miyambo 19:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Wosauka amene akuyenda ndi mtima wosagawanika ali bwino kuposa munthu wa milomo yopotoka,+ komanso munthu wopusa.+
5 Inetu sindingayerekeze n’komwe kunena kuti amuna inu ndinu olungama.+Mpaka ine kumwalira, sindidzasiya kukhala ndi mtima wosagawanika.+
11 Koma ine ndidzayenda mogwirizana ndi mtima wanga wosagawanika.+Ndiwomboleni+ ndi kundikomera mtima.+
12 Koma ine mwandichirikiza chifukwa cha mtima wanga wosagawanika,+Ndipo mudzandiika pamaso panu mpaka kalekale.+
19 Wosauka amene akuyenda ndi mtima wosagawanika ali bwino kuposa munthu wa milomo yopotoka,+ komanso munthu wopusa.+