Nehemiya 13:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Mundikumbukire,+ inu Mulungu wanga, chifukwa cha zinthu zimenezi ndipo musaiwale+ ntchito za kukoma mtima kosatha zimene ndachitira nyumba+ ya Mulungu wanga ndi onse otumikira kumeneko. Salimo 40:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Iye ananditulutsanso m’dzenje la madzi a mkokomo,+Ananditulutsa m’chithaphwi cha matope.+Kenako anapondetsa phazi langa pathanthwe.+Anandiyendetsa panthaka yolimba.+
14 Mundikumbukire,+ inu Mulungu wanga, chifukwa cha zinthu zimenezi ndipo musaiwale+ ntchito za kukoma mtima kosatha zimene ndachitira nyumba+ ya Mulungu wanga ndi onse otumikira kumeneko.
2 Iye ananditulutsanso m’dzenje la madzi a mkokomo,+Ananditulutsa m’chithaphwi cha matope.+Kenako anapondetsa phazi langa pathanthwe.+Anandiyendetsa panthaka yolimba.+