2 Mbiri 24:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Choncho anamuika m’manda a mafumu mu Mzinda wa Davide,+ chifukwa anachita zabwino mu Isiraeli+ ndiponso kwa Mulungu woona ndi nyumba Yake. Salimo 122:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Chifukwa cha nyumba ya Yehova Mulungu wathu,+Ndidzapitiriza kukupempherera kuti zinthu zikuyendere bwino.+
16 Choncho anamuika m’manda a mafumu mu Mzinda wa Davide,+ chifukwa anachita zabwino mu Isiraeli+ ndiponso kwa Mulungu woona ndi nyumba Yake.
9 Chifukwa cha nyumba ya Yehova Mulungu wathu,+Ndidzapitiriza kukupempherera kuti zinthu zikuyendere bwino.+