1 Samueli 18:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Davide anali kuchita zinthu mwanzeru+ nthawi zonse m’njira zake zonse, ndipo Yehova anali naye.+