Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yobu 22:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Tsopano Elifazi wa ku Temani anayankha kuti:

  • Yobu 22:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  5 Kodi kuipa kwako sikwapitirira kale muyezo?+

      Kodi zolakwa zako sizidzatha?

  • Miyambo 27:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Mwana wanga, khala wanzeru ndi kukondweretsa mtima wanga,+ kuti ndimuyankhe amene akunditonza.+

  • Mateyu 24:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 “Kenako anthu adzakuperekani ku chisautso+ ndipo adzakuphani.+ Mitundu yonse idzadana nanu+ chifukwa cha dzina langa.+

  • Chivumbulutso 2:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Usachite mantha ndi mavuto amene ukumane nawo.+ Taona! Mdyerekezi+ adzapitiriza kuponya m’ndende ena a inu, kuti muyesedwe mpaka pamapeto,+ ndipo mudzakhala m’masautso+ masiku 10. Sonyeza kukhulupirika kwako mpaka imfa,+ ndipo ndidzakupatsa mphoto* ya moyo.+

  • Chivumbulutso 6:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Aliyense wa iwo anapatsidwa mkanjo woyera,+ ndipo anauzidwa kuti apumulebe kanthawi pang’ono, kufikira chitakwanira chiwerengero cha akapolo anzawo, ndi abale awo amene anali pafupi kuphedwa+ monga mmene iwonso anaphedwera.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena