Yobu 1:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndiyeno Yehova anafunsanso Satana kuti: “Kodi mtima wako uli pa mtumiki wanga Yobu, poti palibe wina wokhala ngati iyeyo padziko lapansi?+ Iyetu ndi munthu wopanda cholakwa+ ndi wowongoka mtima,+ woopa Mulungu+ ndi wopewa zoipa.”+ Yobu 4:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Takumbukira: Kodi ndani wosalakwa amene anawonongedwapo?Ndipo n’kuti kumene anthu owongoka mtima+ anafafanizidwapo?
8 Ndiyeno Yehova anafunsanso Satana kuti: “Kodi mtima wako uli pa mtumiki wanga Yobu, poti palibe wina wokhala ngati iyeyo padziko lapansi?+ Iyetu ndi munthu wopanda cholakwa+ ndi wowongoka mtima,+ woopa Mulungu+ ndi wopewa zoipa.”+
7 Takumbukira: Kodi ndani wosalakwa amene anawonongedwapo?Ndipo n’kuti kumene anthu owongoka mtima+ anafafanizidwapo?