Deuteronomo 25:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 “Amuna akakangana+ n’kupita kwa oweruza,+ oweruzawo azigamula mlanduwo. Wolungama azimuweruza kuti ndi wolungama ndipo woipa azimuweruza kuti ndi woipa.+ Yobu 40:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Kodi ndithu ukuchititsa chilungamo changa kukhala chopanda pake?Kodi ukunena kuti ine ndine wolakwa kuti iweyo ukhale wolondola?+ Miyambo 17:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Aliyense wonena kuti munthu woipa ndi wolungama+ ndiponso aliyense wonena kuti munthu wolungama ndi woipa,+ onsewa ndi onyansa kwa Yehova.+
25 “Amuna akakangana+ n’kupita kwa oweruza,+ oweruzawo azigamula mlanduwo. Wolungama azimuweruza kuti ndi wolungama ndipo woipa azimuweruza kuti ndi woipa.+
8 Kodi ndithu ukuchititsa chilungamo changa kukhala chopanda pake?Kodi ukunena kuti ine ndine wolakwa kuti iweyo ukhale wolondola?+
15 Aliyense wonena kuti munthu woipa ndi wolungama+ ndiponso aliyense wonena kuti munthu wolungama ndi woipa,+ onsewa ndi onyansa kwa Yehova.+