Ekisodo 23:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 “Usapotoze chigamulo cha munthu wosauka wokhala pakati panu, pa mlandu wake.+ 2 Mbiri 19:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndiyeno anauza oweruzawo kuti: “Samalani zochita zanu+ chifukwa simukuweruzira munthu koma mukuweruzira Yehova,+ ndipo iye ali nanu pa ntchito yoweruzayi.+ Miyambo 17:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Aliyense wonena kuti munthu woipa ndi wolungama+ ndiponso aliyense wonena kuti munthu wolungama ndi woipa,+ onsewa ndi onyansa kwa Yehova.+ Miyambo 31:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Tsegula pakamwa pako, weruza mwachilungamo ndipo thandiza munthu wosautsika ndi wosauka pa mlandu wake.+ Yesaya 5:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Tsoka kwa anthu amene amanena kuti woipa ndi wolungama chifukwa cholandira chiphuphu,+ ndiponso kwa amene amanena kuti wolungama ndi wolakwa.+
6 Ndiyeno anauza oweruzawo kuti: “Samalani zochita zanu+ chifukwa simukuweruzira munthu koma mukuweruzira Yehova,+ ndipo iye ali nanu pa ntchito yoweruzayi.+
15 Aliyense wonena kuti munthu woipa ndi wolungama+ ndiponso aliyense wonena kuti munthu wolungama ndi woipa,+ onsewa ndi onyansa kwa Yehova.+
9 Tsegula pakamwa pako, weruza mwachilungamo ndipo thandiza munthu wosautsika ndi wosauka pa mlandu wake.+
23 Tsoka kwa anthu amene amanena kuti woipa ndi wolungama chifukwa cholandira chiphuphu,+ ndiponso kwa amene amanena kuti wolungama ndi wolakwa.+