Genesis 22:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 ndidzakudalitsa ndithu. Ndiponso ndidzachulukitsadi mbewu yako ngati nyenyezi zakumwamba, monganso mchenga wa m’mphepete mwa nyanja.+ Komanso mbewu yako idzalanda chipata* cha adani ake.+ Genesis 26:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 ‘Ndidzachulukitsa mbewu yako ngati nyenyezi zakumwamba, ndipo mayiko onsewa ndidzawapereka kwa mbewu yako.+ Mitundu yonse ya padziko lapansi idzapeza madalitso*+ ndithu kudzera mwa mbewu yako.’ Genesis 28:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Mbewu yako ndithu idzachuluka ngati mchenga wa padziko lapansi,+ ndipo ana ako adzafalikira kumadzulo, kum’mawa, kumpoto ndi kum’mwera.+ Komanso kudzera mwa iwe ndi mwa mbewu yako, mabanja onse a padziko lapansi adzapeza madalitso*+ ndithu.
17 ndidzakudalitsa ndithu. Ndiponso ndidzachulukitsadi mbewu yako ngati nyenyezi zakumwamba, monganso mchenga wa m’mphepete mwa nyanja.+ Komanso mbewu yako idzalanda chipata* cha adani ake.+
4 ‘Ndidzachulukitsa mbewu yako ngati nyenyezi zakumwamba, ndipo mayiko onsewa ndidzawapereka kwa mbewu yako.+ Mitundu yonse ya padziko lapansi idzapeza madalitso*+ ndithu kudzera mwa mbewu yako.’
14 Mbewu yako ndithu idzachuluka ngati mchenga wa padziko lapansi,+ ndipo ana ako adzafalikira kumadzulo, kum’mawa, kumpoto ndi kum’mwera.+ Komanso kudzera mwa iwe ndi mwa mbewu yako, mabanja onse a padziko lapansi adzapeza madalitso*+ ndithu.