Ekisodo 2:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 M’kupita kwa nthawi, Mulungu anamva+ kubuula kwawo+ ndipo anakumbukira pangano lake ndi Abulahamu, Isaki ndi Yakobo.+ Oweruza 4:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ana a Isiraeli anayamba kulirira Yehova,+ chifukwa Yabini anawapondereza+ kwambiri zaka 20, ndipo iye anali ndi magaleta ankhondo 900 okhala ndi zitsulo zazitali zakuthwa m’mawilo.+ 2 Mafumu 13:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Patapita nthawi Yehoahazi anakhazika pansi+ mtima wa Yehova, kotero kuti Yehova anamumvera,+ popeza anaona kuponderezedwa kwa Aisiraeli,+ chifukwa mfumu ya Siriya inali kuwapondereza.+
24 M’kupita kwa nthawi, Mulungu anamva+ kubuula kwawo+ ndipo anakumbukira pangano lake ndi Abulahamu, Isaki ndi Yakobo.+
3 Ana a Isiraeli anayamba kulirira Yehova,+ chifukwa Yabini anawapondereza+ kwambiri zaka 20, ndipo iye anali ndi magaleta ankhondo 900 okhala ndi zitsulo zazitali zakuthwa m’mawilo.+
4 Patapita nthawi Yehoahazi anakhazika pansi+ mtima wa Yehova, kotero kuti Yehova anamumvera,+ popeza anaona kuponderezedwa kwa Aisiraeli,+ chifukwa mfumu ya Siriya inali kuwapondereza.+