Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Samueli 25:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Choncho Mulungu alange mowirikiza+ adani a Davide, ngati ine ndidzasiya munthu aliyense wa m’nyumba ya Nabala wokodzera khoma*+ ali wamoyo kufikira m’mawa.”+

  • 1 Mafumu 14:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Pa chifukwa chimenechi, ndibweretsa tsoka panyumba ya Yerobowamu. Ndithu ndidzapha munthu aliyense wokodzera khoma*+ wa m’nyumba ya Yerobowamu, ngakhale anthu onyozeka ndi opanda pake mu Isiraeli.+ Komanso ndidzaseseratu nyumba ya Yerobowamu,+ monga momwe munthu amasesera ndowe mpaka atakazitaya.+

  • 2 Mafumu 9:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Nyumba yonse ya Ahabu+ ifafanizidwe. Ine ndidzapha munthu aliyense wokodzera khoma*+ wa m’banja la Ahabu, ngakhale aliyense wonyozeka ndi wopanda pake+ mu Isiraeli.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena