Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Samueli 28:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Choncho Sauli anadzisintha+ ndi kuvala zovala zina. Atatero, iyeyo ndi amuna ena awiri anapita kwa mkaziyo ndipo anafikako usiku.+ Ndiyeno Sauliyo anati: “Ndiloserere zam’tsogolo+ mwa kulankhula ndi mizimu ndipo undiutsire munthu amene ndikuuze.”

  • 2 Samueli 14:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Choncho Yowabu anatumiza anthu ku Tekowa+ kuti akatenge mkazi wanzeru.+ Atabwera naye, Yowabu anamuuza kuti: “Chonde ukhale ngati munthu amene ali panyengo yolira maliro, ndipo uvale zovala za panyengo yolira maliro, komanso usadzole mafuta.+ Ukatero ukhale ngati mkazi amene wakhala akulira maliro kwa masiku ambiri.+

  • 1 Mafumu 22:30
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 30 Tsopano mfumu ya Isiraeli inauza Yehosafati kuti: “Ine ndidzisintha kuti ndisadziwike, ndipo ndimenya nawo nkhondo.+ Koma iweyo uvale zovala zako zachifumu.”+ Chotero mfumu ya Isiraeli inadzisintha+ n’kuyamba kumenya nawo nkhondo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena